Ezekieli 36:28 BL92

28 Ndipo mudzakhala m'dziko ndinapatsa makolo anulo, ndipo mudzakhala anthu anga, ndi Ine ndidzakhala Mulungu wanu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 36

Onani Ezekieli 36:28 nkhani