Ezekieli 36:29 BL92

29 Ndipo ndidzakupulumutsani kwa zodetsa zanu zonse, ndidzaitananso tirigu ndi kumcurukitsa, osaikiranso inu njala.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 36

Onani Ezekieli 36:29 nkhani