Ezekieli 36:35 BL92

35 Ndipo adzati, Dziko ili lacipululu lasanduka ngati munda wa Edene, ndi midzi yamabwinja, ndi yacipululu, ndi yopasuka, yamangidwa malinga, muli anthu m'mwemo.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 36

Onani Ezekieli 36:35 nkhani