Ezekieli 36:36 BL92

36 Pamenepo amitundu otsala pozungulira panu adzadziwa kuti Ine Yehova ndamanga malo opasuka, ndi kubzala pamene panali cipululu; Ine Yehova ndanena ndidzacita.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 36

Onani Ezekieli 36:36 nkhani