Ezekieli 39:25 BL92

25 Cifukwa cace atero Ambuye Yehova, Tsopano ndidzabweza undende wa Yakobo, ndi kucitira cifundo nyumba yonse ya Israyeli, ndipo ndidzacitira dzina langa loyera nsanje.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 39

Onani Ezekieli 39:25 nkhani