Ezekieli 39:26 BL92

26 Ndipo adzasenza manyazi ao, ndi zolakwa zao zonse, zimene anandilakwira nazo, pokhala mosatekeseka iwo m'dziko lao, opanda wina wakuwaopsa;

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 39

Onani Ezekieli 39:26 nkhani