Ezekieli 4:13 BL92

13 Ndipo Yehova anati, Motero ana a Israyeli adz adya ca kudya cao codetsedwa, mwa amitundu kumene ndidzawaingitsirako.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 4

Onani Ezekieli 4:13 nkhani