6 Ndipo utatsiriza awa, ugonerenso mbali yako ya kumanja, ndi kusenza mphulupulu ya nyumba ya Yuda; ndakuikira masiku makumi anai, kuliyesa tsiku limodzi ngati caka cimodzi.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 4
Onani Ezekieli 4:6 nkhani