Ezekieli 4:5 BL92

5 Ndipo Ine ndakuikira zaka za mphulupulu yao ngati masiku, ndiwo masiku mazana atatu mphambu makumi asanu ndi anai, kuti usenze mphulupulu ya nyumba ya Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 4

Onani Ezekieli 4:5 nkhani