Ezekieli 40:23 BL92

23 Ndipo panali cipata ca bwalo lam'kati, copenyana ndi cipata cinzace cakunja kumpoto, ndi ca kum'mawa; ndipo anayesa kuyambira kucipata kufikira kucipata mikono zana.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 40

Onani Ezekieli 40:23 nkhani