Ezekieli 40:24 BL92

24 Ndipo ananditsogolera kumka kumwela, ndipo taonani, panali cipata kumwela, nayesa makhoma a pakati pace, ndi zidundumwa zace, monga mwa miyeso yomweyi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 40

Onani Ezekieli 40:24 nkhani