25 Ndimo munali mazenera m'menemo, ndi m'zidundumwa zace pozungulirapo, monga mazenera ena aja, m'litali mwace mikono makumi asanu, ndi kupingasa kwace mikono makumi awiri mphambu isanu.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 40
Onani Ezekieli 40:25 nkhani