Ezekieli 40:8 BL92

8 Anayesanso khonde la kucipata ku mbali ya kukacisi, bango limodzi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 40

Onani Ezekieli 40:8 nkhani