Ezekieli 41:3 BL92

3 Nalowa m'katimo, nayesa mphuthu za pakhomo mikono iwiri, ndi msinkhu wa khomo mikono isanu ndi umodzi, ndi kupingasa kwa khomo mikono isanu ndi iwiri.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 41

Onani Ezekieli 41:3 nkhani