Ezekieli 41:4 BL92

4 Anayesanso m'kati mwa Kacisi m'tsogolomo, m'litali mwace mikono makumi awiri, ndi kupingasa kwace mikono makumi awiri; ndipo anati kwa ine, Umo m'mopatulikitsa.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 41

Onani Ezekieli 41:4 nkhani