Ezekieli 42:1 BL92

1 Pamenepo anaturuka nane kumka ku bwalo la kunja, njira ya kumpoto; nalowa nane ku nyumba yazipinda idali pandunji pa mpatawo, ndi pandunji pa nyumbayo inaloza kumpoto.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 42

Onani Ezekieli 42:1 nkhani