Ezekieli 41:26 BL92

26 Ndipo panali mazenera a made okhazikika, ndi akanjedza cakuno ndi cauko, kumbali zace za khonde; momwemonso pa zipinda za m'mphepete mwa nyumba, ndi pa matabwa ocindikira.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 41

Onani Ezekieli 41:26 nkhani