Ezekieli 42:5 BL92

5 Ndipo zipinda zapamwamba zinacepa, pakuti makonde am'mwamba analanda pamenepo, cifukwa cace zinacepa koposa zapansi ndi zapakati m'nyumba yazipinda.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 42

Onani Ezekieli 42:5 nkhani