Ezekieli 42:6 BL92

6 Pakuti zinasanjikizana pawiri, ndipo zinalibe nsanamira ngati nsanamira za kumabwalo; cifukwa cace zam'mwambazo zinacepa koposa zakunsi ndi zapakati kuyambira pansi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 42

Onani Ezekieli 42:6 nkhani