Ezekieli 42:7 BL92

7 Ndipo linga linali kunialo, loli'ngana ndi nyumba yazipinda, kuloza ku bwalo lakunja, popenyana ndi nyumba yazipinda, m'litali mwace munali mikono makumi asanu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 42

Onani Ezekieli 42:7 nkhani