19 Upatse ansembe Alevi, a mbeu ya Zadoki, okhala pafupi ndi Ine, kunditumikira Ine, ati Ambuye Yehova, mwana wa ng'ombe, akhale wa nsembe yaucimo.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 43
Onani Ezekieli 43:19 nkhani