Ezekieli 43:20 BL92

20 Nutengeko mwazi wace, ndi kupaka pa nyanga zinai za guwa, ndi pa ngondya zinai za phaka, ndi pa mkuzi wace pozungulira; motero uliyeretse ndi kulicitira cotetezera.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 43

Onani Ezekieli 43:20 nkhani