Ezekieli 44:13 BL92

13 Ndipo asayandikire kwa Ine kundigwirira nchito ya nsembe, kapena kuyandikira zopatulika zanga ziri zonse zopatulikitsazo; koma azisenza manyazi ao, ndi zonyansa zao anazicita.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 44

Onani Ezekieli 44:13 nkhani