Ezekieli 44:18 BL92

18 Akhale nao akapa abafuta pamitu pao, ndi akabudula m'cuuno mwao; asabvale m'cuuno kanthu kali konse kakucititsa thukuta.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 44

Onani Ezekieli 44:18 nkhani