Ezekieli 44:22 BL92

22 Kungakhale kutenga amasiye kapena osudzulidwa akhale akazi ao, asacite; koma atenge anamwali a mbeu ya nyumba ya Israyeli, kapena wamasiye ndiye wamasiye wa wansembe.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 44

Onani Ezekieli 44:22 nkhani