Ezekieli 44:23 BL92

23 Ndipo aziphunzitsa anthu anga asiyanitse pakati pa zopatulika ndi zinthu wamba, ndi kuwazindikiritsa pakati pa zodetsa ndi zoyera.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 44

Onani Ezekieli 44:23 nkhani