9 Atero Ambuye Yehova, Palibe mlendo wosadulidwa m'mtima, wosadulidwa m'thupi, alowe m'malo anga opatulika, mwa alendo onse ali pakati pa ana a Israyeli.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 44
Onani Ezekieli 44:9 nkhani