Ezekieli 44:8 BL92

8 Ndipo simunasunga udikiro wa zopatulika zanga, koma mwadziikira mokha osunga udikiro wanga m'malo anga opatulika.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 44

Onani Ezekieli 44:8 nkhani