Ezekieli 46:21 BL92

21 Pamenepo anaturukira nane ku bwalo lakunja, nandipititsa ku ngondya zinai za bwaloli; ndipo taonani, m'ngondya monse munali bwalo.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 46

Onani Ezekieli 46:21 nkhani