22 M'ngondya zinai za bwalo munali mabwalo ocingika, m'litali mwace mikono makumi anai, kupingasa kwace makumi atatu; awa anai m'ngondyazi analingana muyeso wace.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 46
Onani Ezekieli 46:22 nkhani