Ezekieli 46:5 BL92

5 ndi nsembe yaufa ikhale efa wa pa nkhosa yamphongo, ndi nsembe ya ufa wa pa ana a nkhosa, monga akhoza kupatsa; ndi hini a wa mafuta wa paefa.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 46

Onani Ezekieli 46:5 nkhani