Ezekieli 47:13 BL92

13 Atero Ambuye Yehova, Malire amene mugawe nao dziko likhale colowa cao monga mwa mafuko khumi ndi awiri a Israyeli ndi awa: Yosefe akhale nao magawo awiri.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 47

Onani Ezekieli 47:13 nkhani