14 Ndipo mudzakhala nalo colowa canu wina ndi mnzace yemwe, ndilo limene ndinakwezapo dzanja langa kulipereka kwa makolo anu, ndi dziko ili lidzakugwerani colowa canu.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 47
Onani Ezekieli 47:14 nkhani