Ezekieli 47:19 BL92

19 Ndi mbali ya kumwela kuloza kumwela ndiyo kuyambira ku Tamara kufikira ku madzi a Meriboti Kadesi, ku mtsinje wa Aigupto, ndi ku nyanja yaikuru. Ndiyo mbali ya kumwela kuloza kumwela.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 47

Onani Ezekieli 47:19 nkhani