Ezekieli 47:20 BL92

20 Ndi mbali ya kumadzulo ndiyo nyanja yaikuru, kuyambira malire a kumwela kufikira pandunji polowera ku Hamati. Ndiyo mbali ya kumadzulo.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 47

Onani Ezekieli 47:20 nkhani