11 Atero Yehova Mulungu, Omba manja ako, ponda ndi phazi lako, nuti, Kalanga ine, cifukwa ca zonyansa zoipa zonse za nyumba ya Israyeli; pakuti adzagwa ndi lupanga, ndi njala, ndi mliri.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 6
Onani Ezekieli 6:11 nkhani