Ezekieli 6:12 BL92

12 Wokhala kutali adzafa ndi mliri, wakhala pafupi adzagwa ndi lupanga; koma wotsala ndi kuzingidwa adzafa ndi njala; momwemo ndidzawakwaniritsira ukali wanga,

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 6

Onani Ezekieli 6:12 nkhani