Ezekieli 7:15 BL92

15 Kunja kuli lupanga, ndi m'katimo muli mliri ndi njala; wokhala kuthenso adzafa ndi lupanga, ndi wokhala m'mudziyo njala ndi mliri zidzamutha.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 7

Onani Ezekieli 7:15 nkhani