Ezekieli 7:16 BL92

16 Ndipo akupulumuka mwa iwo adzapulumuka, koma adzakhala kumapiri ngati njiwa za kuzigwa, onse akubuula, ali yense m'mphulupulu zace.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 7

Onani Ezekieli 7:16 nkhani