21 Ndipo ndidzacipereka m'dzanja la alendo cikhale colandika, ndi kwa oipa a m'dziko cikhale cofunkha; ndipo adzaciipsa.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 7
Onani Ezekieli 7:21 nkhani