20 Ndipo cokometsera cace cokongola anaciyesa codzikuza naco, napanga naco mafanizo ao onyansa, ndi zonyansa zao zina; cifukwa cace ndinapatsa ici cikhale cowadetsa.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 7
Onani Ezekieli 7:20 nkhani