Ezekieli 7:27 BL92

27 Mfumu idzalira maliro, ndi kalonga adzabvala cipasuko, ndi manja a anthu a m'dziko adzanjenjemera, Ndidzawacitira monga mwa njira zao, ndi kuwaweruza monga mwa maweruzo ao; ndipo adzadziwa kuti Ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 7

Onani Ezekieli 7:27 nkhani