Ezekieli 7:8 BL92

8 Katsala kamphindi, ndipo ndidzakutsanulira ukali wanga, ndi kukukwaniritsira mkwiyo wanga, ndi kukuweruza monga mwa njira zako, ndipo ndidzakubwezera zonyansa zako zonse.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 7

Onani Ezekieli 7:8 nkhani