Ezekieli 7:9 BL92

9 Ndipo diso langa silidzalekerera, wosacita cifundo Ine, ndidzakubwezera monga mwa njira zako, ndi zonyansa zako zidzakhala pakati pako; ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova wakukantha.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 7

Onani Ezekieli 7:9 nkhani