Ezekieli 8:4 BL92

4 Ndipo taonani, pomwepo panali ulemerero wa Mulungu wa lsrayeli, monga mwa maonekedwe ndinawaona ku cidikha cija.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 8

Onani Ezekieli 8:4 nkhani