Ezekieli 9:11 BL92

11 Ndipo taonani, munthu wobvala bafutayo, wokhala ndi zolembera nazo m'cuuno mwace, anabweza mau, ndi kuti, Ndacita monga munandilamulira ine.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 9

Onani Ezekieli 9:11 nkhani