Ezekieli 10:1 BL92

1 Ndipo ndinapenya, ndipo taonani, ku thambo lokhala pamwamba pa mitu ya akerubi kudaoneka ngati mwala wasafiro, ngati maonekedwe a cifaniziro ca mpando wacifumu pamwamba pao.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 10

Onani Ezekieli 10:1 nkhani