6 Amene akhetsa mwazi wa munthu, ndi munthunso mwazi wace udzakhetsedwa: cifukwa m'cifanizo ca Mulungu Iye anampanga munthu.
Werengani mutu wathunthu Genesis 9
Onani Genesis 9:6 nkhani