Ezekieli 16:18 BL92

18 Unatenganso zobvala zako za nsaru yopikapika, ndi kuwabveka nazo, unaikanso mafuta anga ndi cofukiza canga pamaso pao.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 16

Onani Ezekieli 16:18 nkhani