Ezekieli 17:10 BL92

10 Inde ungakhale waokedwa udzakondwa kodi? sudzauma ciumire kodi pakuuomba mphepo ya kum'mawa? udzauma pookedwa apo udaphuka.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 17

Onani Ezekieli 17:10 nkhani